Warm Heart of Africa Letra

The Very Best

Otras Canciones

Letra de Warm Heart of Africa
Is hip-hop hereditary?
I don't know
Oh, the boys move fast
You should take it slow
Well, we all need someone to tell us when to go
A beat-box imaginary in the show
All you shell-toes lined up in a row
All your favorite breaks
Your favorite ELO

Musadabwe ndikamavina ine gule wakwathu uuuu
Kum'mwera kwa Africa kule dziko limodzi lotchedwa
Malawi iiii
Warm heart of Africa kuli magule magule okoma aaaa
Tchopa, manganje, ngoma, vimbuza, maseche ndi
M'ganda aaaa

Zikomo zikomo nonse
Kodi muli bwanji
Ine ndili bwino ooooo
Alendo asaononge
Dziko la mtendere
Malawi wabwino ooooo

Zikatere zikatere tiyeni tilowe m'bwalo
Zikatere zikatere wayaka moto oo
Zikatere zikatere pali ngozi pano
Zikatere zikatere malawi moto oo

Oh please tell me when to go
Iwe newo