Very Best (The)

Mwazi
Ukakhala iwe mphwangaUsadzinamize uli ndi abaleAmakukonda uli ndi chumaUkasauka kukutayaAmayiwala kuti mwazi ndi mwaziUmawundana kuposa madziIwe iwe mveraTchera tchera khutuGaniza ngati munthu From Letras Mania